Mwazi Songtext

Ukakhala iwe mphwanga
Usadzinamize uli ndi abale
Amakukonda uli ndi chuma
Ukasauka kukutaya
Amayiwala kuti mwazi ndi mwazi
Umawundana kuposa madzi

Iwe iwe mvera
Tchera tchera khutu
Ganiza ngati munthu

Mwazi Video

Mwazi Video play
This website uses cookies to ensure you get the best experience on our website. Closing this message or scrolling the page you will allow us to use it. Learn more